Pakwathu Entertainment

Pakwathu Entertainment 🎭 Your home of entertainment! Bringing you the latest trending news, comedy, music, viral videos, and inspiring content from Malawi and beyond.

Follow, like, and share

Sad newsπŸ’”Ku thyolo kasaila village T/A mphukaZatimvuta kubanja lathu la magogoda mayi F***y Nyasa amene amaziwika ndizin...
22/08/2026

Sad newsπŸ’”
Ku thyolo kasaila village T/A mphuka
Zatimvuta kubanja lathu la magogoda mayi F***y Nyasa amene amaziwika ndizina loti Anagama atisiya usiku wathawu

21/08/2026

With Pakwathu Entertainment – I just made it onto their weekly engagement list by being one of their top engagers!

19/08/2026

Mayina amabwana kusililitsa mpaka akuti pwepweteπŸ˜ƒπŸ’˜πŸ“Œ

19/08/2026

Muli bwanji akazi ogula nokha malo nkumangapo nyumba?πŸ˜„πŸ«΅

19/08/2026

Si basi mudamuluza mamuna wa vision uja achisilu inu πŸ€”πŸ€”

19/08/2026

Kodi zakhalanso bwanji za ?😊

Naye Osaka ndalama akati atuwe ngati samakhala ndi ndalamatu
19/08/2026

Naye Osaka ndalama akati atuwe ngati samakhala ndi ndalamatu

Kodi   mutu wake muli nzeru bhobho kapena ine ndikungomuda bas Ali bhobho?????πŸ˜…πŸ«΅
19/08/2026

Kodi mutu wake muli nzeru bhobho kapena ine ndikungomuda bas Ali bhobho?????πŸ˜…πŸ«΅

19/08/2026

Shout out to my newest followers! Excited to have you onboard! Rohan Bihari Vloger, Mfura Mdingi, Tshepisang D Matlhole, Yah Mie

18/08/2026

Muli bwanji akazi okhala nokha pa rent??πŸ˜…πŸ«΅

Address

Chileka

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when Pakwathu Entertainment posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share