The ROAD TRIP

The ROAD TRIP Modern Bars, Live Band & Jazz, Coffee & Ice-Cream Shop, Restaurant & Swimming Pool

Stay a while, make it worthy the trip

Eni Khomo.Nthawi ya ma samoosas sagwirikatu😋❤️Crispy, tasty, and enjoyed one bite at a time.Thank you for choosing The R...
19/10/2026

Eni Khomo.
Nthawi ya ma samoosas sagwirikatu😋❤️

Crispy, tasty, and enjoyed one bite at a time.
Thank you for choosing The RoadTrip. 🫶🏽

Samoosa wathuyu ambiri akupereka feedback yabwino kwabasi 🔥 🔥

18/10/2026
18/10/2026

Live band yatentha eeeh. 🎶🔥❤️

Ku mlakho konko 🔥😂Eeeh abale ....... Zinthu zake... 😅
18/10/2026

Ku mlakho konko 🔥😂
Eeeh abale ....... Zinthu zake... 😅

18/10/2026

Weekend timalize ndi LIVE BAND! Eni Khomo, musasowe — tikuwoneni lero ku RoadTrip🎤

Pali funso lachanguchangu apa, dress code mwayiwona? Nanga Mwakonzeka?Tizayiwonetse photo booth kulakwa kwake 🔥👗
18/10/2026

Pali funso lachanguchangu apa, dress code mwayiwona? Nanga Mwakonzeka?

Tizayiwonetse photo booth kulakwa kwake 🔥👗

Ticket isakupelewereni, this is the right time to buy, masiku nde akupita.

Koma dress code yo mwaiwona? 🩷💛🤍

Uku ma MaxSherrians tikakhale pamodzi tikaipatse moto ku The ROAD TRIP

18/10/2026

From ku Mlakho straight ku The RoadTrip lero 😂🔥

18/10/2026

Sunday si tsiku longothamangitsa ma file.
Pumani, sangalalani, ndipo lero khalani ndi anthu amene amakupatsani mtendere. ❤️

🧡  Eni Khomo, ABWERE  🧡💃🏽This Sunday, 18th Oct — SUNSET SESSIONS 🎶 3PM till late. IYIYI Musayiphonye 🚀
17/10/2026

🧡 Eni Khomo, ABWERE 🧡💃🏽
This Sunday, 18th Oct — SUNSET SESSIONS 🎶

3PM till late. IYIYI Musayiphonye 🚀

Address

Chiradzulu
Blantyre

Website

Alerts

Be the first to know and let us send you an email when The ROAD TRIP posts news and promotions. Your email address will not be used for any other purpose, and you can unsubscribe at any time.

Shortcuts

Share

Category